1 Petro 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu wa cisomo conse, amene adakuitanani kulowa ulemerero wace wosatha mwa Kristu, mutamva zowawa kanthawi, adzafikitsa inu opanda cirema mwini wace, adzakhazikitsa, adzalimbikitsa inu.

1 Petro 5

1 Petro 5:5-14