1 Mbiri 9:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ena a iwo anaikidwa ayang'anire zipangizo ziti zonse, ndi zipangizo zonse za malo opatulika, ndi ufa wosalala, ndi vinyo, ndi mafuta, ndi libano, ndi zonunkhira.

1 Mbiri 9

1 Mbiri 9:24-31