1 Mbiri 9:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amagona usiku m'zipinda zozinga nyumba ya Mulungu, popeza udikiro wace ndi wao; kuitsegula m'mawa ndi m'mawa ndi kwaonso.

1 Mbiri 9

1 Mbiri 9:26-30