1 Mbiri 9:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Salumu mwana wa Kore, mwana wa Ebiasafu; mwana wa Kora, ndi abale ace a nyumba ya atate wace; Akora anayang'anira nchito ya utumiki, osunga zipata za kacisi monga makolo ao; anakhala m'cigono ca Yehova osunga polowera;

1 Mbiri 9

1 Mbiri 9:12-28