1 Mbiri 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi abale ao, akuru a nyumba za makolo ao cikwi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi limodzi, anthu odziwitsitsa Debito ya utumiki wa nyumba ya Mulungu.

1 Mbiri 9

1 Mbiri 9:11-15