1 Mbiri 8:3-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ndi Bela anali ndi ana: Adara, ndi Gera, ndi Abihudi,

4. ndi Abisuwa, ndi Namani, ndi Ahowa,

5. ndi Gera, ndi Sefufani, ndi Huramu.

6. Ndi ana a Ehudi ndi awa: ndiwo akuru a nyumba za makolo ao a iwo okhala ku Geba, ndipo anawatenga ndende kumka ku Manahati,

7. natenga ndende Namani, ndi Ahiya, ndi Gera, ndipo, anabala Uza, ndi Ahihudi.

8. Ndipo Saharaimu anabala ana ku dziko la Moabu, atacotsa akazi ace Husimu ndi Baara.

9. Ndipo Hodesi mkazi wace anambalira Yohabu, ndi Zibiya, ndi Mesa, ndi Malikamu,

10. ndi Yeuzi, ndi Sakiya, ndi Mirima. Awa ndi ana ace akurua nyumbazamakolo ao.

11. Ndi Husimu anambalira Abitubu, ndi Elipaala.

12. Ndi ana a Elipaala: Eberi, ndi Misamu, ndi Semedi, amene anamanga Ono, ndi Ludi ndi miraga yace,

13. ndi Beriya, ndi Sema; ndiwo akuru a nyumba za makolo a iwo okhala m'Ayaloni, amene anathawitsa okhala m'Gati;

14. ndi Ahio, Sasaki, ndi Yeremoti,

15. ndi Zebadiya, ndi Aradi, ndi Ederi,

16. ndi Mikaeli, ndi Isipa, ndi Yoha, ana a Beriya;

17. ndi Zebadiya, ndi Mesulamu, ndi Hiziki, ndi Heberi,

18. ndi Ismerai, ndi Izliya, ndi Yobabu, ana a Elipaala;

19. ndi Yakimu, ndi Zikiri, ndi Zabidi,

1 Mbiri 8