1 Mbiri 8:23-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. ndi Abidoni, ndi Zikiri, ndi Hanani,

24. ndi Hananiya, ndi Elamu, ndi Antotiya,

25. ndi Ifideya, ndi Penueli, ana a Sasaki;

26. ndi Samserai, ndi Sehariya, ndi Ataliya,

27. ndi Yaaresiya ndi Eliya, ndi Zikiri, ana a Yerohamu.

28. Awa ndi akuru a nyumba za makolo mwa mibadwo yao, ndiwo akuru anakhala m'Yerusalemu awa.

29. Ndipo m'Gibeoni anakhala atate a Gibeoni, dzina la mkazi wace ndiye Maaka;

30. ndi mwana wace woyamba ndiye Abidoni, opondana naye ndi Zuri, ndi Kisi, ndi Baala, ndi Nadabu,

31. ndi Gedoro, ndi Ahiyo, ndi Zekeri.

1 Mbiri 8