1 Mbiri 7:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Maaka mkazi wa Makiri anabala mwana, namucha dzina lace Peresi, ndi dzina la mbale wace ndiye Seresi, ndi ana ace ndiwo Ulamu, ndi Rakemu.

1 Mbiri 7

1 Mbiri 7:6-25