1 Mbiri 6:77 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Otsala a Alevi analandira, motapa pa pfuko la Zebuluni, Rimono ndi mabusa ace, Tabora ndi mabusa ace;

1 Mbiri 6

1 Mbiri 6:73-81