1 Mbiri 6:65 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapatsa mwamaere, motapa pa pfuko la ana a Yuda, ndi pa pfuko la Simeoni, ndi pa pfuko la ana a Benjamini, midzi iyi yochulidwa maina ao.

1 Mbiri 6

1 Mbiri 6:55-66