1 Mbiri 6:63 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana a Merari analandira mwa maere monga mwa mabanja ao, motapa pa pfuko la Rubeni, ndi pa pfuko la Gadi, ndi pa pfuko la Zebuluni, midzi khumi ndi iwiri.

1 Mbiri 6

1 Mbiri 6:59-65