1 Mbiri 6:6-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. ndi Uzi anabala Zerahiya, ndi Zerahiya anabala Merayoti,

7. Merayoti anabala Amariya, ndi Amariya anabala Ahitubu,

8. ndi Ahitubu anabala Zadoki, ndi Zadoki anabala Ahimaazi,

9. ndi Ahimaazi anabala Azariya, ndi Azariya anabala Yohanani,

1 Mbiri 6