1 Mbiri 6:43-46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. mwana wa Yabati, mwana wa Gerisomu, mwana wa Levi.

44. Ndi ku dzanja lamanzere abale ao ana a Merari: Etani mwana wa Kisi, mwana wa Abidi, mwana wa Maluki,

45. mwana wa Hasabiya, mwana wa Amaziya, mwana wa Hilikiya,

46. mwana wa Amzi, mwana wa Bani, mwana wa Semeri,

1 Mbiri 6