1 Mbiri 6:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Eliabu mwana wace, Yerohamu mwana wace, Elikana mwana wace. Ndi ana a Samueli: woyamba Yoeli, ndi waciwiri Abiya.