1 Mbiri 6:15-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. ndi Yehozadaki analowa undende muja Yehova anatenga ndende Yuda ndi Yerusalemu ndi dzanja la Nebukadinezara.

16. Ana a Levi: Gerisomu, Kohati ndi Merari.

17. Ndipo maina a ana a Gerisomu ndi awa: Libni, ndi Simei.

18. Ndipo ana a Kohati ndiwo Amramu, ndi lzara, ndi Hebroni, ndi Uzieli.

19. Ana a Merari: Mali ndi Musi. Ndi mabanja a Alevi monga mwa nyumba za makolo ao ndi awa.

20. Wa Gerisomu: Libni mwana wace, Yahati mwana wace, Zina mwana wace,

1 Mbiri 6