1 Mbiri 5:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ana a limodzi la magawo awiri a pfuko la Manase anakhala m'dziko; anacuruka kuyambira Basana kufikira Baala Herimoni, ndi Seniri, ndi phiri la Herimoni.

1 Mbiri 5

1 Mbiri 5:17-26