1 Mbiri 5:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analanda zoweta zao, ngamila zao zikwi makumi asanu, ndi nkhosa zikwi mazana awiri ndi makumi asanu, ndi aburu zikwi ziwiri, ndi amuna zikwi zana limodzi.

1 Mbiri 5

1 Mbiri 5:17-25