1 Mbiri 5:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onsewo anawerengedwa monga mwa mabuku a cibadwidwe cao, masiku a Yotamu mfumu ya Yuda, ndi m'masiku a Yerobiamu mfumu ya Israyeli.

1 Mbiri 5

1 Mbiri 5:11-22