1 Mbiri 4:31-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. ndi ku Betimarikaboti, ndi ku Hazarasusimu, ndi ku Betibiri, ndi ku Saraimu. Iyi ndi midzi yao, mpaka ufumu wa Davide, pamodzi ndi miraga yao.

32. Etamu, ndi Aini, Rimoni, ndi Tokeni, ndi Asani, midzi isanu;

33. ndi miraga yao yonse pozungulira pace pa midzi yomweyi, mpaka Baala. Apo ndi pokhala pao ndipo ali nao mawerengedwe a maina ao.

1 Mbiri 4