1 Mbiri 4:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Simei anali nao ana amuna khumi mphambu asanu ndi mmodzi, ndi ana akazi asanu ndi mmodzi; koma abale ace analibe ana ambiri, ndi banja lao lonse silinacurukitsa ngati ana a Yuda.

1 Mbiri 4

1 Mbiri 4:17-30