1 Mbiri 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mkazi wace Myuda anabala Yeredi atate wa Gedoro, ndi Heberi atate wa Soko, ndi Yekutiyeli atate wa Zanowa. Ndipo awa ndi ana a Bitiya mwana wamkazi wa Farao, amene Meredi anamtenga.

1 Mbiri 4

1 Mbiri 4:9-22