1 Mbiri 29:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amene anali nayo miyala ya mtengo wace anaipereka ku cuma ca nyumba ya Yehova, mwa dzanja la Yehieli Mgerisoni.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:6-15