1 Mbiri 29:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso popeza ndikondwera nayo nyumba ya Mulungu wanga, cuma cangacanga ca golidi ndi siliva ndiri naco ndicipereka ku nyumba ya Mulungu wanga, moenjezera ndi zonse ndazikonzeratu nyumba yopatulikayo;

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:1-13