1 Mbiri 29:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nadya namwa pamaso pa Mulungu tsiku lomwelo ndi cimwemwe cacikuru. Ndipo analonga ufumu Solomo mwana wa Davide kaciwiri, namdzozera Yehova akhale kalonga, ndi Zadoki akhale wansembe.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:17-30