1 Mbiri 29:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nimupatse Solomo mwana wanga mtima wangwiro kusunga malamulo anu, mboni zanu, ndi malemba anu, ndi kucita izi zonse, ndi kumanga cinyumbaci cimene ndakonzeratu mirimo yace,

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:9-21