1 Mbiri 29:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidziwanso, Mulungu wanga, kuti muyesa mtima, nimukondwera nako kuongoka. Kama ine, ndi mtima wanga woongoka ndapereka zonsezi mwaufulu; ndipo tsopano ndaona mokondwera anthu anu okhala pompano, napereka kwa Inu mwaufulu.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:10-22