1 Mbiri 28:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi cifaniziro ca zonse anali nazo mwa mzimu, ca mabwalo a nyumba ya Yehova, ndi ca zipinda zonse pozungulirapo, ca zosungiramo cuma za nyumba ya Mulungu, ndi ca zosungiramo cuma za zinthu zopatulika;

1 Mbiri 28

1 Mbiri 28:10-15