1 Mbiri 27:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wacinai wa mwezi wacinai ndiye Asebeli mbale wa Yoabu, ndi pambuyo pace Zebadiya mwana wace; ndi m'cigawo mwace munali zikwi makumi awiri mphambu zinai.

1 Mbiri 27

1 Mbiri 27:4-10