1 Mbiri 27:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kazembe wacitatu wa khamu wa mwezi wacitatu ndiye Benaya mwana wa Yehoyada wansembe wamkuru; ndi m'cigawo mwacemunalinso zikwi makumi awiri mphambu zinai.

1 Mbiri 27

1 Mbiri 27:1-6