1 Mbiri 27:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi woyang'anira mitengo yaazitona, ndi yamikuyu yokhala kuzidikha kunsi, ndiye Baala Hanani Mgederi; ndi woyang'anira zosungiramo mafuta ndiye Yoasi;

1 Mbiri 27

1 Mbiri 27:21-33