1 Mbiri 26:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onsewa ndiwo a ana a Obedi Edomu; iwo ndi ana ao, ndi abale ao, anthu odziwa mphamvu yakutumikira, makumi asanu ndi limodzi mphambu awiri a Obedi Edomu.

1 Mbiri 26

1 Mbiri 26:1-16