1 Mbiri 26:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Hosa yemwe wa ana a Merari anali ndi ana, wamkuru ndi Simri; pakuti ngakhale sanali wobadwa woyamba, atate wace anamuyesa wamkuru;

1 Mbiri 26

1 Mbiri 26:7-14