1 Mbiri 25:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Onsewa anawalangiza ndi atate wao ayimbe m'nyumba ya Yehova ndi nsanje, zisakasa ndi azeze; atumikire nazo m'nyumba ya Mulungu; ndipo Asafu, Yedutuni, ndi Hemani, anawalangiza ndi mfumu.

1 Mbiri 25

1 Mbiri 25:1-7