1 Mbiri 23:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Davide anati, Yehova Mulungu wa Israyeli wapumulitsa anthu ace; ndipo akhala m'Yerusalemu kosatha;

1 Mbiri 23

1 Mbiri 23:24-26