1 Mbiri 22:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati asonkhanitse alendo okhala m'dziko la Israyeli; iye naika osema miyala afukule miyala, aiseme kuti amange nayo nyumba ya Mulungu.

1 Mbiri 22

1 Mbiri 22:1-8