1 Mbiri 21:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mfumu Davide anati kwa Orinani, lai, koma ndidzaligula pa mtengo wace wonse; pakuti sindidzatengera Yehova ciri cako, kapena kupereka nsembe yopsereza yopanda mtengo wace.

1 Mbiri 21

1 Mbiri 21:20-28