1 Mbiri 21:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Davide tsono anati kwa Orinani, Ndipatse padwale pano kuti ndimangepo guwa la nsembe la Yehova; undipatse gi pa mtengo wace wonse, kuti mliri ulekeke pa anthu.

1 Mbiri 21

1 Mbiri 21:14-30