1 Mbiri 21:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa Yoabu ndi kwa akuru a anthu, Kawerengeni Israyeli kuyambira ku Beereseba kufikira ku Dani; nimundibwezere mau, kuti ndidziwe ciwerengo cao.

1 Mbiri 21

1 Mbiri 21:1-5