1 Mbiri 21:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anatuma mthenga ku Yerusalemu kuuononga; ndipo poti auononge, Yehova anapenya, naleka coipaci; nati kwa mthenga wakuononga, Cakwanira, bweza dzanja lako tsopano. Ndi mthenga wa Yehova anaima pa dwale la Orinani Myebusi,

1 Mbiri 21

1 Mbiri 21:7-22