1 Mbiri 21:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa Gadi, Ndipsinjika kwambiri; ndigwere m'dzanja la Yehova, pakuti zifundo zace zicurukadi; koma ndisagwere m'dzanja la munthu.

1 Mbiri 21

1 Mbiri 21:5-23