1 Mbiri 20:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panalinso nkhondo ndi Afgisti; ndi Elihanani mwana wa Yairi anapha Lami mbale wa Goliati Mgiti, amene luti la mkondo wace linanga mtanda woombera nsaru.

1 Mbiri 20

1 Mbiri 20:1-8