1 Mbiri 20:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anatenga korona wa mfumu yao kumcotsa pamutu pace, napeza kulemera kwace talente wa golidi; panalinso miyala ya mtengo wace pamenepo; ndipo anamuika pamutu pa Davide, naturutsa zankhondo za m'mudzimo zambiri ndithu.

1 Mbiri 20

1 Mbiri 20:1-6