1 Mbiri 2:37-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

37. ndi Zabadi anabala Efilali, ndi Efilali anabala Obedi,

38. ndi Obedi anabala Yehu, ndi Yehu anabala Azariya,

39. ndi Azariya anabala Helezi, ndi Helezi anabala Eleasa,

40. ndi Eleasa anabala Sismai, ndi Sismai anabala Salumu,

1 Mbiri 2