1 Mbiri 19:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anadzilembera magareta zikwi makumi atatu mphambu ziwiri, ndi mfumu ya Maaka ndi anthu ace; nadza iwo, namanga misasa cakuno ca Medeba. Ana a Amoni omwe anasonkhana m'midzi mwao, nadza kunkhondo.

1 Mbiri 19

1 Mbiri 19:2-15