1 Mbiri 19:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuona Aaramu kuti Israyeli anawakantha, anatumiza mithenga, naturuka nao Aaramu akukhala tsidya lija la mtsinjewo; ndi Sofaki kazembe wa khamu la Hadarezeri anawatsogolera.

1 Mbiri 19

1 Mbiri 19:8-19