1 Mbiri 18:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ku Tibati, ndi ku Kuni, midzi ya Hadarezeri, Davide anatenga mkuwa wambiri, ndiwo umene Solomo anayenga nao thawale lamkuwa, ndi nsanamira, ndi zipangizo zamkuwa.

1 Mbiri 18

1 Mbiri 18:3-11