1 Mbiri 18:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Izi zomwe mfumu Davide anazipatulira Yehova, pamodzi ndi siliva ndi golidi adazitenga kwa amitundu onse, kwa Edomu, ndi kwa Moabu, ndi kwa ana a Amoni, ndi kwa Afilisti, ndi kwa Amaleki.

1 Mbiri 18

1 Mbiri 18:10-17