1 Mbiri 18:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo zitatha izi, Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa, nalanda Gati ndi midzi yace m'manja a Afilisti.

2. Anakanthanso Moabu; ndi Amoabu anakhala anthu a Davide, nabwera nazo mphatso,

1 Mbiri 18