1 Mbiri 17:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ndipo usiku womwewo mau a Mulungu anadzera Natani, ndi kuti,

4. Kauze Davide mtumiki wanga, Atero Yehova, Usandimangire nyumba yokhalamo;

5. pakuti sindinakhala m'nyumba kuyambira tsiku tija ndinakwera naye Israyeli, kufikira lero Gno; koma wa m'hema m'hema Ine, ndi wa m'kacisi m'kacisi,

1 Mbiri 17