1 Mbiri 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu Davide analowa nakhala pamaso pa Yehova, nati, Ndine yani, Yehova Mulungu, ndi nyumba yanga njotani kuti mwandifikitsa mpaka pano?

1 Mbiri 17

1 Mbiri 17:12-21